-
2 Samueli 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Choncho Tamara anapita kunyumba kwa mchimwene wake Aminoni, ndipo anamupeza atagona. Ndiyeno anakanda ufa nʼkuumba makeke Aminoniyo akuona, kenako anawaphika.
-