2 Samueli 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Aminoni anauza Tamara kuti: “Bweretsa chakudya* kuchipinda kuno kuti ndidye chili mʼmanja mwako.” Choncho Tamara anatenga makeke amene anaphikawo nʼkupita nawo kwa mchimwene wake Aminoni kuchipinda.
10 Ndiyeno Aminoni anauza Tamara kuti: “Bweretsa chakudya* kuchipinda kuno kuti ndidye chili mʼmanja mwako.” Choncho Tamara anatenga makeke amene anaphikawo nʼkupita nawo kwa mchimwene wake Aminoni kuchipinda.