-
2 Samueli 13:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kodi ine ndizikhala bwanji zimenezi zikachitika? Komanso Aisiraeli azikuonani ngati munthu woipa komanso wochititsa manyazi. Lankhulani ndi mfumu, chifukwa sangakukanizeni kuti munditenge.”
-