-
2 Samueli 13:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Aminoni atachita zimenezo anayamba kudana naye kwambiri. Anadana naye kwambiri kuposa mmene ankamukondera, moti anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita!”
-