-
2 Samueli 13:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma Tamara anamuyankha kuti: “Ayi achimwene, musatero. Kundithamangitsa panopa nʼkoipa kwambiri kuposa zimene mwachitazi!” Koma Aminoni sanamumvere.
-