-
2 Samueli 13:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 (Tamara anali atavala mkanjo wapadera umene ankavala ana aakazi a mfumu omwe anali anamwali.) Choncho mtumiki wake uja anamutulutsa nʼkukhoma chitseko.
-