2 Samueli 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Tamara anadzithira phulusa kumutu+ ndiponso kungʼamba mkanjo umene anavala uja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu nʼkunyamuka kumapita, akulira.
19 Kenako Tamara anadzithira phulusa kumutu+ ndiponso kungʼamba mkanjo umene anavala uja. Ndiyeno anaika manja ake pamutu nʼkunyamuka kumapita, akulira.