2 Samueli 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu Davide atamva zimene zinachitikazo, anakwiya kwambiri.+ Koma sanafune kukhumudwitsa mwana wake Aminoni chifukwa ankamukonda popeza anali woyamba kubadwa. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:21 Nsanja ya Olonda,12/15/2015, tsa. 17
21 Mfumu Davide atamva zimene zinachitikazo, anakwiya kwambiri.+ Koma sanafune kukhumudwitsa mwana wake Aminoni chifukwa ankamukonda popeza anali woyamba kubadwa.