2 Samueli 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patatha zaka ziwiri, antchito a Abisalomu ankameta ubweya wa nkhosa ku Baala-hazori, pafupi ndi Efuraimu.+ Ndipo Abisalomu anaitana ana onse aamuna a mfumu.+
23 Patatha zaka ziwiri, antchito a Abisalomu ankameta ubweya wa nkhosa ku Baala-hazori, pafupi ndi Efuraimu.+ Ndipo Abisalomu anaitana ana onse aamuna a mfumu.+