-
2 Samueli 13:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Abisalomu anapita kwa mfumu nʼkunena kuti: “Ine mtumiki wanu, antchito anga akumeta ubweya wa nkhosa. Ndikupempha kuti inu mfumu ndi atumiki anu mupite nane limodzi.”
-