-
2 Samueli 13:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Koma mfumu inayankha Abisalomu kuti: “Ayi mwana wanga. Tikapita tonse, tikakuvutitsa.” Ngakhale kuti Abisalomu anachondererabe, mfumuyo sinalole kupita koma inamudalitsa.
-