2 Samueli 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Abisalomu anati: “Poti inuyo simupita, ndikupempha kuti mchimwene wanga Aminoni apite nafe.”+ Mfumu inamufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukufuna kuti apite nawe?”
26 Kenako Abisalomu anati: “Poti inuyo simupita, ndikupempha kuti mchimwene wanga Aminoni apite nafe.”+ Mfumu inamufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukufuna kuti apite nawe?”