2 Samueli 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho atumiki a Abisalomu anapha Aminoni mogwirizana ndi zimene Abisalomuyo anawalamula. Zitatero, ana onse a mfumu ananyamuka ndipo aliyense anakwera nyulu* yake nʼkuthawa.
29 Choncho atumiki a Abisalomu anapha Aminoni mogwirizana ndi zimene Abisalomuyo anawalamula. Zitatero, ana onse a mfumu ananyamuka ndipo aliyense anakwera nyulu* yake nʼkuthawa.