-
2 Samueli 13:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Mfumu itamva zimenezi inaimirira nʼkungʼamba zovala zake ndipo inagona pansi. Atumiki ake onse anaimirira pafupi ndi mfumuyo nawonso atangʼamba zovala zawo.
-