32 Koma Yehonadabu+ mwana wa Simeya,+ mchimwene wake wa Davide anati: “Mbuyanga, musaganize kuti ana onse a mfumu aphedwa, Aminoni yekha ndi amene wafa+ ndipo walamula zimenezi ndi Abisalomu. Iye anaganiza zochita zimenezi+ kuyambira tsiku limene Aminoniyo anagwiririra mchemwali wake+ Tamara.+