-
2 Samueli 13:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Mbuyanga mfumu, musamvere zimene akunenazi zoti, ‘Ana onse a mfumu afa.’ Amene wafa ndi Aminoni yekha.”