2 Samueli 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pa nthawiyi nʼkuti Abisalomu atathawa.+ Kenako mlonda wina, atakweza maso anaona anthu ambiri akubwera kumbuyo kwake mumsewu umene unali pafupi ndi phiri.
34 Pa nthawiyi nʼkuti Abisalomu atathawa.+ Kenako mlonda wina, atakweza maso anaona anthu ambiri akubwera kumbuyo kwake mumsewu umene unali pafupi ndi phiri.