-
2 Samueli 14:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Tonsefe tidzafa ndipo tidzakhala ngati madzi otayika amene sawoleka. Koma Mulungu satenga moyo ndipo amaganizira zifukwa zoti munthu amene wathamangitsidwa asakhalebe wothamangitsidwa.
-