-
2 Samueli 14:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Mtumiki wanu Yowabu wachita zimenezi kuti musinthe mmene mukuonera nkhaniyi. Koma inu mbuyanga muli ndi nzeru ngati mngelo wa Mulungu woona, moti mukudziwa zonse zimene zikuchitika mʼdzikoli.”
-