-
2 Samueli 14:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Yowabu atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi ndipo anatamanda mfumu. Yowabu anati: “Ine mtumiki wanu ndadziwa kuti lero mwandikomera mtima, mbuyanga mfumu, chifukwa inu mfumu mwamvera zimene ine mtumiki wanu ndapempha.”
-