-
2 Samueli 14:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Koma mfumu inanena kuti: “Apite kunyumba kwake, asaonane nane.” Choncho Abisalomu anapita kunyumba kwake, ndipo sanaonane ndi mfumu.
-