-
2 Samueli 14:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Mu Isiraeli munalibe mwamuna amene anthu ankamuona kuti ndi wooneka bwino kwambiri koposa Abisalomu. Iye analibe chilema chilichonse kuyambira kuphazi mpaka pamutu.
-