-
2 Samueli 14:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Zitatero, Abisalomu anauza atumiki ake kuti: “Pafupi ndi munda wanga pali munda wa Yowabu ndipo muli balere. Mupite mukautenthe.” Choncho atumiki a Abisalomu anapita nʼkukawotchadi mundawo.
-