2 Samueli 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho Yowabu anapita kwa mfumu nʼkukanena mawu amenewa. Ndiyeno mfumu inaitanitsa Abisalomu ndipo iye anapita. Atafika anagwada nʼkuwerama, kenako anadzigwetsa pansi pamaso pa mfumu. Zitatero, mfumu inamukisa Abisalomu.+
33 Choncho Yowabu anapita kwa mfumu nʼkukanena mawu amenewa. Ndiyeno mfumu inaitanitsa Abisalomu ndipo iye anapita. Atafika anagwada nʼkuwerama, kenako anadzigwetsa pansi pamaso pa mfumu. Zitatero, mfumu inamukisa Abisalomu.+