2 Samueli 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Abisalomu anapeza galeta lokokedwa ndi mahatchi komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+
15 Kenako Abisalomu anapeza galeta lokokedwa ndi mahatchi komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+