-
2 Samueli 15:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Abisalomu ankanenanso kuti: “Zikanakhala bwino ndikanaikidwa kukhala woweruza mʼdzikoli. Bwenzi ndikuonetsetsa kuti munthu aliyense amene wabwera ndi mlandu kwa ine, wachitiridwa chilungamo.”
-