2 Samueli 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso munthu akafika pafupi kuti amuweramire, Abisalomu ankamugwira nʼkumuletsa ndipo kenako ankamukisa.+
5 Komanso munthu akafika pafupi kuti amuweramire, Abisalomu ankamugwira nʼkumuletsa ndipo kenako ankamukisa.+