2 Samueli 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abisalomu ankachita zimenezi kwa Aisiraeli onse amene ankabwera kwa mfumu kuti awaweruzire milandu yawo. Choncho Abisalomu anapitiriza kukopa anthu mu Isiraeli.+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:6 Nsanja ya Olonda,7/15/2012, tsa. 13
6 Abisalomu ankachita zimenezi kwa Aisiraeli onse amene ankabwera kwa mfumu kuti awaweruzire milandu yawo. Choncho Abisalomu anapitiriza kukopa anthu mu Isiraeli.+