2 Samueli 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine mtumiki wanu pamene ndinali ku Gesuri,+ ku Siriya ndinalonjeza+ kuti: ‘Yehova akandilola kubwerera ku Yerusalemu, ndidzapereka nsembe kwa* Yehova.’”
8 Ine mtumiki wanu pamene ndinali ku Gesuri,+ ku Siriya ndinalonjeza+ kuti: ‘Yehova akandilola kubwerera ku Yerusalemu, ndidzapereka nsembe kwa* Yehova.’”