-
2 Samueli 15:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mfumu inamuyankha kuti: “Pita mwamtendere.” Zitatero, ananyamuka nʼkupita ku Heburoni.