2 Samueli 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Abisalomu anatumiza akazitape ku mafuko onse a Isiraeli ndipo anawauza kuti: “Mukangomva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, mufuule kuti, ‘Tsopano Abisalomu ndi mfumu ku Heburoni!’”+
10 Ndiyeno Abisalomu anatumiza akazitape ku mafuko onse a Isiraeli ndipo anawauza kuti: “Mukangomva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, mufuule kuti, ‘Tsopano Abisalomu ndi mfumu ku Heburoni!’”+