-
2 Samueli 15:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pochoka ku Yerusalemu, Abisalomu anatenga amuna 200. Anthuwa anawaitana ndipo anapita mʼchimbulimbuli osadziwa chilichonse.
-