2 Samueli 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho mfumu inanyamuka limodzi ndi anthu onse amʼnyumba yake. Koma mfumuyo inasiya akazi ake aangʼono*+ 10, kuti azisamalira nyumba.*
16 Choncho mfumu inanyamuka limodzi ndi anthu onse amʼnyumba yake. Koma mfumuyo inasiya akazi ake aangʼono*+ 10, kuti azisamalira nyumba.*