2 Samueli 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atumiki onse a mfumu amene ananyamuka nawo limodzi, Akereti onse, Apeleti+ onse, Agiti+ onse ndiponso amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anayamba kudutsa kutsogolo kwa mfumuyo kuti idziwe anthu amene alipo.
18 Ndiyeno atumiki onse a mfumu amene ananyamuka nawo limodzi, Akereti onse, Apeleti+ onse, Agiti+ onse ndiponso amuna 600 amene anamutsatira* kuchokera ku Gati+ anayamba kudutsa kutsogolo kwa mfumuyo kuti idziwe anthu amene alipo.