2 Samueli 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe wabwera dzulodzuloli, ndiye lero uyambe kuyendayenda ndi ife nʼkumapita kumene ine ndikupita? Bwerera, utengenso abale akowa ndipo Yehova akusonyeze chikondi komanso kukhulupirika kwake!”+
20 Iwe wabwera dzulodzuloli, ndiye lero uyambe kuyendayenda ndi ife nʼkumapita kumene ine ndikupita? Bwerera, utengenso abale akowa ndipo Yehova akusonyeze chikondi komanso kukhulupirika kwake!”+