2 Samueli 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma Itai anayankha mfumu kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo komanso mbuyanga mfumu muli apa, kulikonse kumene inu mungapite, ine mtumiki wanu ndipitanso komweko, ndipo ndine wokonzeka ngakhale kufa nanu limodzi!”+
21 Koma Itai anayankha mfumu kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo komanso mbuyanga mfumu muli apa, kulikonse kumene inu mungapite, ine mtumiki wanu ndipitanso komweko, ndipo ndine wokonzeka ngakhale kufa nanu limodzi!”+