2 Samueli 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zadoki+ nayenso anali komweko limodzi ndi Alevi+ onse atanyamula likasa+ la pangano la Mulungu woona.+ Aleviwo anatula pansi Likasa la Mulungu woona ndipo Abiyatara+ anali pomwepo mpaka anthu onse anamaliza kudutsa kuchokera mumzinda.
24 Zadoki+ nayenso anali komweko limodzi ndi Alevi+ onse atanyamula likasa+ la pangano la Mulungu woona.+ Aleviwo anatula pansi Likasa la Mulungu woona ndipo Abiyatara+ anali pomwepo mpaka anthu onse anamaliza kudutsa kuchokera mumzinda.