2 Samueli 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumu inauza Zadoki wansembe kuti: “Paja iwe ndiwe wamasomphenya.+ Iwe ndi Abiyatara bwererani kumzinda mwamtendere. Mubwerere pamodzi ndi ana anu awiri, Ahimazi mwana wako wamwamuna ndi Yonatani+ mwana wamwamuna wa Abiyatara.
27 Mfumu inauza Zadoki wansembe kuti: “Paja iwe ndiwe wamasomphenya.+ Iwe ndi Abiyatara bwererani kumzinda mwamtendere. Mubwerere pamodzi ndi ana anu awiri, Ahimazi mwana wako wamwamuna ndi Yonatani+ mwana wamwamuna wa Abiyatara.