2 Samueli 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamene Davide ankakwera phiri la Maolivi,+ ankalira komanso anaphimba kumutu. Iye ankayenda wopanda nsapato ndipo anthu onse amene anali naye nawonso anaphimba kumutu ndipo ankalira.
30 Pamene Davide ankakwera phiri la Maolivi,+ ankalira komanso anaphimba kumutu. Iye ankayenda wopanda nsapato ndipo anthu onse amene anali naye nawonso anaphimba kumutu ndipo ankalira.