2 Samueli 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Davide atafika pamwamba pa phiri, pomwe anthu ankapita kukalambira Mulungu, anaona Husai+ mbadwa ya Areki+ akubwera kudzakumana naye, atangʼamba mkanjo wake ndiponso atadzithira dothi kumutu.
32 Davide atafika pamwamba pa phiri, pomwe anthu ankapita kukalambira Mulungu, anaona Husai+ mbadwa ya Areki+ akubwera kudzakumana naye, atangʼamba mkanjo wake ndiponso atadzithira dothi kumutu.