2 Samueli 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma ubwerere kumzinda ndipo ukauze Abisalomu kuti, ‘Mfumu, ine ndine mtumiki wanu. Poyamba ndinali mtumiki wa bambo anu koma tsopano ndine mtumiki wanu.’+ Ukakatero, ukatha kunditsutsira malangizo a Ahitofeli.+
34 Koma ubwerere kumzinda ndipo ukauze Abisalomu kuti, ‘Mfumu, ine ndine mtumiki wanu. Poyamba ndinali mtumiki wa bambo anu koma tsopano ndine mtumiki wanu.’+ Ukakatero, ukatha kunditsutsira malangizo a Ahitofeli.+