2 Samueli 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zadoki ndi Abiyatara omwe ndi ansembe ali komweko. Chilichonse chimene ukamve kunyumba ya mfumu ukauze Zadoki ndi Abiyatara.+
35 Zadoki ndi Abiyatara omwe ndi ansembe ali komweko. Chilichonse chimene ukamve kunyumba ya mfumu ukauze Zadoki ndi Abiyatara.+