2 Samueli 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Iwo alinso ndi ana awo awiri komweko, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Ndiye mukatume ana awowo kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.”
36 Iwo alinso ndi ana awo awiri komweko, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Ndiye mukatume ana awowo kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.”