2 Samueli 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Choncho Husai, mnzake wa Davide,+ anapita ku Yerusalemu pa nthawi imene Abisalomu ankalowa mumzindawu.
37 Choncho Husai, mnzake wa Davide,+ anapita ku Yerusalemu pa nthawi imene Abisalomu ankalowa mumzindawu.