2 Samueli 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako mfumu inafunsa kuti: “Nanga mwana* wa mbuye wako ali kuti?”+ Ziba anauza mfumu kuti: “Watsala ku Yerusalemu ndipo wanena kuti, ‘Lero nyumba ya Isiraeli indibwezera ufumu wa bambo anga.’”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:3 Nsanja ya Olonda,2/15/2002, ptsa. 14-15
3 Kenako mfumu inafunsa kuti: “Nanga mwana* wa mbuye wako ali kuti?”+ Ziba anauza mfumu kuti: “Watsala ku Yerusalemu ndipo wanena kuti, ‘Lero nyumba ya Isiraeli indibwezera ufumu wa bambo anga.’”+