2 Samueli 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mfumu inauza Ziba kuti: “Zinthu zonse zimene zinali za Mefiboseti zikhale zako.”+ Ziba anati: “Ulemu wanu mfumu. Pitirizani kundikomera mtima mbuyanga mfumu.”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2018, tsa. 6
4 Kenako mfumu inauza Ziba kuti: “Zinthu zonse zimene zinali za Mefiboseti zikhale zako.”+ Ziba anati: “Ulemu wanu mfumu. Pitirizani kundikomera mtima mbuyanga mfumu.”+