2 Samueli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumu Davide itafika ku Bahurimu, mwamuna wina wa mʼbanja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera anatulukira akulankhula mawu onyoza.+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2018, ptsa. 6-7
5 Mfumu Davide itafika ku Bahurimu, mwamuna wina wa mʼbanja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera anatulukira akulankhula mawu onyoza.+