2 Samueli 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wakubwezera mlandu wa magazi a nyumba ya Mfumu Sauli amene iwe unamulowa mʼmalo. Yehova wapereka ufumu mʼmanja mwa Abisalomu mwana wako. Ndipo tsoka lakugwera chifukwa uli ndi mlandu wa magazi!”+
8 Yehova wakubwezera mlandu wa magazi a nyumba ya Mfumu Sauli amene iwe unamulowa mʼmalo. Yehova wapereka ufumu mʼmanja mwa Abisalomu mwana wako. Ndipo tsoka lakugwera chifukwa uli ndi mlandu wa magazi!”+