2 Samueli 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Abisai mwana wa Zeruya+ anauza mfumu kuti: “Nʼchifukwa chiyani galu wakufayu+ akukunyozani mbuyanga mfumu?+ Bwanji ndipite ndikamʼdule mutu?”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:9 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, tsa. 32
9 Kenako Abisai mwana wa Zeruya+ anauza mfumu kuti: “Nʼchifukwa chiyani galu wakufayu+ akukunyozani mbuyanga mfumu?+ Bwanji ndipite ndikamʼdule mutu?”+