2 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Davide ndi amuna amene anali naye anapitiriza ulendo wawo. Simeyi ankayenda mʼmbali mwa phiri pafupi ndi Davide, uku akulankhula mawu onyoza,+ kugenda ndi miyala ndiponso kuwaza fumbi lambiri.
13 Choncho Davide ndi amuna amene anali naye anapitiriza ulendo wawo. Simeyi ankayenda mʼmbali mwa phiri pafupi ndi Davide, uku akulankhula mawu onyoza,+ kugenda ndi miyala ndiponso kuwaza fumbi lambiri.